Genesis 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Leya anati: “Ndachita mwayi!” Chotero anatcha mwanayo dzina lakuti Gadi.*+ Genesis 46:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ana a Gadi+ anali Zifioni, Hagi, Suni, Eziboni, Eri, Arodi ndi Areli.+ Numeri 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana aamuna a Gadi+ ndi mabanja awo anali awa: Zefoni amene anali kholo la banja la Azefoni, Hagi amene anali kholo la banja la Ahagi, Suni amene anali kholo la banja la Asuni,
15 Ana aamuna a Gadi+ ndi mabanja awo anali awa: Zefoni amene anali kholo la banja la Azefoni, Hagi amene anali kholo la banja la Ahagi, Suni amene anali kholo la banja la Asuni,