Genesis 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Rakele anati: “Ndalimbana mwamphamvu ndi m’bale wanga ndipo ndapambananso.” Chotero anatcha mwanayo dzina lakuti Nafitali.*+ Genesis 46:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ana a Nafitali+ anali Yahazeeli, Guni,+ Yezera ndi Silemu.+ Numeri 26:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ana aamuna a Nafitali+ ndi mabanja awo anali awa: Yahazeeli+ amene anali kholo la banja la Ayahazeeli, Guni+ amene anali kholo la banja la Aguni,
8 Ndiyeno Rakele anati: “Ndalimbana mwamphamvu ndi m’bale wanga ndipo ndapambananso.” Chotero anatcha mwanayo dzina lakuti Nafitali.*+
48 Ana aamuna a Nafitali+ ndi mabanja awo anali awa: Yahazeeli+ amene anali kholo la banja la Ayahazeeli, Guni+ amene anali kholo la banja la Aguni,