Numeri 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo ana a Isiraeli nawonso anayamba kulira n’kumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+ Numeri 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tikukumbukira nsomba zaulere zimene tinali kudya ku Iguputo,+ nkhaka, mavwende, adyo komanso anyezi wamitundumitundu!
4 Tsopano khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo ana a Isiraeli nawonso anayamba kulira n’kumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+
5 Tikukumbukira nsomba zaulere zimene tinali kudya ku Iguputo,+ nkhaka, mavwende, adyo komanso anyezi wamitundumitundu!