Ekisodo 29:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa nkhosa yolongera Aroni ndi ana ake unsembe,+ upatule nganga+ ya nsembe yoweyula imene anaweyula, ndi mwendo wa gawo lopatulika umene anapereka. Levitiko 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nganga ya nsembe yoweyula+ ndiponso mwendo, umene ndi gawo lopatulika, ndikuzitenga pansembe zachiyanjano za ana a Isiraeli. Ndikuzitenga kwa ana a Isiraeli ndi kuzipereka kwa Aroni wansembe ndi ana ake. Ili ndi lamulo mpaka kalekale.
27 Pa nkhosa yolongera Aroni ndi ana ake unsembe,+ upatule nganga+ ya nsembe yoweyula imene anaweyula, ndi mwendo wa gawo lopatulika umene anapereka.
34 Nganga ya nsembe yoweyula+ ndiponso mwendo, umene ndi gawo lopatulika, ndikuzitenga pansembe zachiyanjano za ana a Isiraeli. Ndikuzitenga kwa ana a Isiraeli ndi kuzipereka kwa Aroni wansembe ndi ana ake. Ili ndi lamulo mpaka kalekale.