Genesis 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mbewu yako ndithu idzachuluka ngati mchenga wa padziko lapansi,+ ndipo ana ako adzafalikira kumadzulo, kum’mawa, kumpoto ndi kum’mwera.+ Komanso kudzera mwa iwe ndi mwa mbewu yako, mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso*+ ndithu. Deuteronomo 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Yehova Mulungu wako akadzafutukula malire a dziko lako+ monga mmene wakulonjezera,+ ndipo iwe n’kudzanena kuti, ‘Ndikufuna kudya nyama,’ chifukwa walakalaka kudya nyama, nthawi iliyonse imene mtima wako walakalaka kudya nyama uzidzadya.+
14 Mbewu yako ndithu idzachuluka ngati mchenga wa padziko lapansi,+ ndipo ana ako adzafalikira kumadzulo, kum’mawa, kumpoto ndi kum’mwera.+ Komanso kudzera mwa iwe ndi mwa mbewu yako, mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso*+ ndithu.
20 “Yehova Mulungu wako akadzafutukula malire a dziko lako+ monga mmene wakulonjezera,+ ndipo iwe n’kudzanena kuti, ‘Ndikufuna kudya nyama,’ chifukwa walakalaka kudya nyama, nthawi iliyonse imene mtima wako walakalaka kudya nyama uzidzadya.+