Salimo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngakhale gulu lankhondo litamanga msasa kuti lindiukire,+Mtima wanga sudzachita mantha.+Ngakhale nkhondo yolimbana ndi ine itayambika,+Pameneponso ndidzadalira Mulungu.+ Yesaya 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene ali ndi nkhawa mumtima mwawo muwauze kuti:+ “Limbani mtima.+ Musachite mantha.+ Pakuti Mulungu wanu adzabwera n’kudzabwezera adani anu.+ Mulungu adzabwezera chilango.+ Iye adzabwera n’kukupulumutsani.”+ Yesaya 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+
3 Ngakhale gulu lankhondo litamanga msasa kuti lindiukire,+Mtima wanga sudzachita mantha.+Ngakhale nkhondo yolimbana ndi ine itayambika,+Pameneponso ndidzadalira Mulungu.+
4 Amene ali ndi nkhawa mumtima mwawo muwauze kuti:+ “Limbani mtima.+ Musachite mantha.+ Pakuti Mulungu wanu adzabwera n’kudzabwezera adani anu.+ Mulungu adzabwezera chilango.+ Iye adzabwera n’kukupulumutsani.”+
10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+