1 Samueli 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa tsiku limeneli Sauli sananene chilichonse, pakuti mumtima mwake anaganiza kuti: “China chake chachitika, ayenera kuti wadetsedwa,+ ndipo sanayeretsedwe.”
26 Pa tsiku limeneli Sauli sananene chilichonse, pakuti mumtima mwake anaganiza kuti: “China chake chachitika, ayenera kuti wadetsedwa,+ ndipo sanayeretsedwe.”