Numeri 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+ Numeri 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero Miriamu anatulutsidwa kukakhala kunja kwa msasa masiku 7,+ ndipo anthuwo sanasamuke kufikira Miriamu atalandiridwanso mumsasa.
10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+
15 Chotero Miriamu anatulutsidwa kukakhala kunja kwa msasa masiku 7,+ ndipo anthuwo sanasamuke kufikira Miriamu atalandiridwanso mumsasa.