-
2 Samueli 18:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Tsopano Abisalomu akali moyo anadzimangira chipilala.+ Chipilala chimenechi chili m’Chigwa cha Mfumu,+ pakuti iye anati: “Ine ndilibe mwana wamwamuna woti asunge dzina langa monga chikumbukiro.”+ Choncho chipilala chimenecho anachitcha dzina lake+ ndipo chikudziwikabe ndi dzina lakuti Chipilala cha Abisalomu kufikira lero.
-