1 Samueli 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Samueli anadzuka m’mawa kwambiri kuti akaonane ndi Sauli. Koma uthenga unam’peza Samueli wonena kuti: “Sauli anabwera ku Karimeli,+ ndipotu waimika chipilala+ cha chikumbutso chake, kenako watembenuka ndipo wapita ku Giligala.”
12 Kenako Samueli anadzuka m’mawa kwambiri kuti akaonane ndi Sauli. Koma uthenga unam’peza Samueli wonena kuti: “Sauli anabwera ku Karimeli,+ ndipotu waimika chipilala+ cha chikumbutso chake, kenako watembenuka ndipo wapita ku Giligala.”