Ekisodo 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Muzitumikira Yehova Mulungu wanu,+ ndipo adzakudalitsani ndi chakudya ndi madzi.+ Ndipo ndidzachotsa matenda pakati panu.+ Salimo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pulumutsani anthu anu, ndipo dalitsani cholowa chanu.+Mukhale m’busa wawo ndipo muwanyamule mpaka kalekale.+ Salimo 115:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova watikumbukira, ndipo adzapereka madalitso,+Adzadalitsa nyumba ya Isiraeli,+Adzadalitsa nyumba ya Aroni.+
25 Muzitumikira Yehova Mulungu wanu,+ ndipo adzakudalitsani ndi chakudya ndi madzi.+ Ndipo ndidzachotsa matenda pakati panu.+
9 Pulumutsani anthu anu, ndipo dalitsani cholowa chanu.+Mukhale m’busa wawo ndipo muwanyamule mpaka kalekale.+
12 Yehova watikumbukira, ndipo adzapereka madalitso,+Adzadalitsa nyumba ya Isiraeli,+Adzadalitsa nyumba ya Aroni.+