Deuteronomo 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Motero muzimvera mawu a Yehova Mulungu wanu, mwa kusunga malamulo ake+ onse amene ndikukupatsani lero, kuti muzichita zinthu zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wanu.+ Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.
18 Motero muzimvera mawu a Yehova Mulungu wanu, mwa kusunga malamulo ake+ onse amene ndikukupatsani lero, kuti muzichita zinthu zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wanu.+
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.