Genesis 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ndidzakwaniritsa pangano langa la pakati pa ine ndi iwe,+ ndi mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe ku mibadwomibadwo. Lidzakhala pangano mpaka kalekale,+ kusonyeza kuti ndine Mulungu wako ndi wa mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe.+ Ekisodo 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.” Deuteronomo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu+ kuti akulanditseni m’nyumba yaukapolo,+ m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani,+ komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+ Aheberi 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu,+ analumbira pa dzina lake+ chifukwa panalibe wina wamkulu kwa iye amene akanamulumbirira.
7 “Ndidzakwaniritsa pangano langa la pakati pa ine ndi iwe,+ ndi mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe ku mibadwomibadwo. Lidzakhala pangano mpaka kalekale,+ kusonyeza kuti ndine Mulungu wako ndi wa mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe.+
6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.”
8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu+ kuti akulanditseni m’nyumba yaukapolo,+ m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani,+ komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+
13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu,+ analumbira pa dzina lake+ chifukwa panalibe wina wamkulu kwa iye amene akanamulumbirira.