Deuteronomo 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 ndipo mudzalandira temberero+ limeneli ngati simudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ n’kupatuka panjira imene ndikukulamulani lero kuti muziyendamo, n’kuyamba kutsatira milungu ina imene simukuidziwa. Salimo 119:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwadzudzula odzikuza otembereredwa,+Amene akusochera ndi kuchoka pa malamulo anu.+ Yeremiya 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma iwo sanamvere kapena kutchera khutu,+ ndipo anapitiriza kuyenda mwa zofuna zawo, mwa kuuma kwa mtima wawo woipawo,+ mwakuti anali kuyenda mobwerera m’mbuyo osati mopita patsogolo,+
28 ndipo mudzalandira temberero+ limeneli ngati simudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ n’kupatuka panjira imene ndikukulamulani lero kuti muziyendamo, n’kuyamba kutsatira milungu ina imene simukuidziwa.
24 Koma iwo sanamvere kapena kutchera khutu,+ ndipo anapitiriza kuyenda mwa zofuna zawo, mwa kuuma kwa mtima wawo woipawo,+ mwakuti anali kuyenda mobwerera m’mbuyo osati mopita patsogolo,+