Nehemiya 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+ Yesaya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+ anthu olemedwa ndi zolakwa, mbewu yochita zoipa,+ ana obweretsa chiwonongeko.+ Iwo amusiya Yehova.+ Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu,+ ndipo abwerera m’mbuyo.+ Yeremiya 32:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anali kundifulatira, sanandiyang’ane.+ Ngakhale kuti ndinali kuwaphunzitsa, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwaphunzitsa, palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene anamvetsera kuti alandire mwambo.*+
26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+
4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+ anthu olemedwa ndi zolakwa, mbewu yochita zoipa,+ ana obweretsa chiwonongeko.+ Iwo amusiya Yehova.+ Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu,+ ndipo abwerera m’mbuyo.+
33 Iwo anali kundifulatira, sanandiyang’ane.+ Ngakhale kuti ndinali kuwaphunzitsa, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwaphunzitsa, palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene anamvetsera kuti alandire mwambo.*+