Ekisodo 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chotero nyumba ya Isiraeli inayamba kutcha chakudyacho kuti “mana.”* Chinali choyera ngati njere ya mapira,* ndipo kukoma kwake kunali ngati makeke opyapyala othira uchi.+ Salimo 78:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.+Iye anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+
31 Chotero nyumba ya Isiraeli inayamba kutcha chakudyacho kuti “mana.”* Chinali choyera ngati njere ya mapira,* ndipo kukoma kwake kunali ngati makeke opyapyala othira uchi.+
24 Ndipo anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.+Iye anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+