11 “Pitani mumsasa wonsewu, mukauze anthu kuti, ‘Konzekani ndi kutenga zonse zofunikira, chifukwa pakapita masiku atatu kuchokera lero, mudzawoloka Yorodano uyu, ndi kulowa m’dzikolo kuti mukalilande, dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu.’”+