Genesis 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iyi ndi nkhani yofotokoza mmene kumwamba ndi dziko lapansi zinalengedwera, m’tsiku limene Yehova Mulungu anapanga dziko lapansi ndi kumwamba.+ Yeremiya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+
4 Iyi ndi nkhani yofotokoza mmene kumwamba ndi dziko lapansi zinalengedwera, m’tsiku limene Yehova Mulungu anapanga dziko lapansi ndi kumwamba.+
10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+