1 Mafumu 8:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 inuyo mumve muli kumwamba,+ malo anu okhala okhazikika+ ndipo mukhululuke+ ndi kuchitapo kanthu.+ Mupatse aliyense malinga ndi njira zake zonse,+ popeza mukudziwa mtima wake+ (popeza inuyo nokha mumadziwa bwino mtima wa ana onse a anthu).+ Salimo 139:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mumandidziwa bwino pamene ndikuyenda komanso pamene ndikugona,+Ndipo njira zanga zonse mukuzidziwa bwino.+ Yeremiya 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mumandidziwa bwino.+ Mumandiona ndipo mumasanthula mtima wanga kuti muone ngati uli wokhulupirika kwa inu.+ Apatuleni ngati nkhosa zimene zikukaphedwa,+ ndipo aikeni padera kuyembekezera tsiku lokaphedwa.
39 inuyo mumve muli kumwamba,+ malo anu okhala okhazikika+ ndipo mukhululuke+ ndi kuchitapo kanthu.+ Mupatse aliyense malinga ndi njira zake zonse,+ popeza mukudziwa mtima wake+ (popeza inuyo nokha mumadziwa bwino mtima wa ana onse a anthu).+
3 Mumandidziwa bwino pamene ndikuyenda komanso pamene ndikugona,+Ndipo njira zanga zonse mukuzidziwa bwino.+
3 Inu Yehova, mumandidziwa bwino.+ Mumandiona ndipo mumasanthula mtima wanga kuti muone ngati uli wokhulupirika kwa inu.+ Apatuleni ngati nkhosa zimene zikukaphedwa,+ ndipo aikeni padera kuyembekezera tsiku lokaphedwa.