Salimo 103:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova wakhazikitsa mpando wake wachifumu kumwamba.+Ndipo ufumu wake ukulamulira chilichonse.+ Mateyu 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Wolumbirira kumwamba walumbirira mpando wachifumu wa Mulungu+ komanso amene akukhala pampandowo.