Genesis 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anamutengera panja, n’kumuuza kuti: “Kweza maso ako kumwamba, uwerenge nyenyezizo ngati ungathe kuziwerenga.”+ Ndipo anamuuzanso kuti: “Umu ndi mmene mbewu yako idzakhalire.”+ Aroma 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anali ndi chiyembekezo ndiponso chikhulupiriro+ chakuti adzakhala tate wa mitundu yambiri,+ ngakhale kuti zimenezi zinkaoneka kuti n’zosatheka. Anakhulupirira zimenezi mogwirizana ndi zimene zinanenedwa kuti: “Umu ndi mmene mbewu yako idzakhalire.”+ Aheberi 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anati: “Kudalitsa, ndidzakudalitsa ndithu, ndipo ndidzakuchulukitsadi.”+
5 Kenako anamutengera panja, n’kumuuza kuti: “Kweza maso ako kumwamba, uwerenge nyenyezizo ngati ungathe kuziwerenga.”+ Ndipo anamuuzanso kuti: “Umu ndi mmene mbewu yako idzakhalire.”+
18 Anali ndi chiyembekezo ndiponso chikhulupiriro+ chakuti adzakhala tate wa mitundu yambiri,+ ngakhale kuti zimenezi zinkaoneka kuti n’zosatheka. Anakhulupirira zimenezi mogwirizana ndi zimene zinanenedwa kuti: “Umu ndi mmene mbewu yako idzakhalire.”+