Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Tsopano ndikukutumizira mngelo+ wokutsogolera kuti akuteteze m’njira ndi kukakulowetsa m’dziko limene ndakukonzera.+

  • 1 Mafumu 22:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mikaya anapitiriza kunena kuti: “Choncho imvani mawu a Yehova:+ Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu,+ makamu onse akumwamba ataimirira kudzanja lake lamanja ndi kumanzere kwake.+

  • Salimo 103:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tamandani Yehova, inu angelo+ ake amphamvu, ochita zimene wanena,+

      Mwa kumvera malamulo ake.+

  • Salimo 148:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mutamandeni, inu angelo ake onse.+

      Mutamandeni, inu khamu lake lonse.+

  • Danieli 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma kalonga+ wa ufumu wa Perisiya+ ananditsekereza+ kwa masiku 21, ndipo Mikayeli,+ mmodzi mwa akalonga aakulu+ anabwera kudzandithandiza, ndipo pa nthawi imeneyo ndinakhalabe pafupi ndi mafumu a Perisiya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena