Yoswa 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ankhondo onse+ amene anali limodzi ndi Yoswa anapita naye, n’kukafika pafupi ndi mzindawo kutsogolo kwake. Atafika anamanga msasa kumpoto kwa Ai, ndipo pakati pa iwo ndi mzindawo panali chigwa.
11 Ankhondo onse+ amene anali limodzi ndi Yoswa anapita naye, n’kukafika pafupi ndi mzindawo kutsogolo kwake. Atafika anamanga msasa kumpoto kwa Ai, ndipo pakati pa iwo ndi mzindawo panali chigwa.