Yoswa 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Yehova anauza Yoswa kuti: “Usaope kapena kuchita mantha.+ Tenga amuna onse ankhondo. Nyamuka, upite kudziko la Ai. Taona, mfumu ya Ai ndaipereka m’manja mwako limodzi ndi anthu ake, mzinda wake, ndi dziko lake.+ Yoswa 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho, Yoswa limodzi ndi amuna onse ankhondo+ anakonzeka kupita ku Ai. Yoswa anasankha amuna okwanira 30,000, asilikali amphamvu ndi olimba mtima,+ n’kuwatumiza usiku.
8 Tsopano Yehova anauza Yoswa kuti: “Usaope kapena kuchita mantha.+ Tenga amuna onse ankhondo. Nyamuka, upite kudziko la Ai. Taona, mfumu ya Ai ndaipereka m’manja mwako limodzi ndi anthu ake, mzinda wake, ndi dziko lake.+
3 Choncho, Yoswa limodzi ndi amuna onse ankhondo+ anakonzeka kupita ku Ai. Yoswa anasankha amuna okwanira 30,000, asilikali amphamvu ndi olimba mtima,+ n’kuwatumiza usiku.