Yoswa 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo, asilikali amene anabisala aja anavumbuluka pamalo pamene anali. Pa nthawi imene iye anatambasula dzanja lake, iwo anathamanga n’kukalowa mumzindawo n’kuulanda.+ Atatero, anauyatsa moto mzindawo mofulumira.+ Yoswa 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chotero Yoswa anatentha mzinda wa Ai+ n’kuusiya uli bwinja lokhalapo mpaka kalekale, ndipo lilipobe mpaka lero.
19 Pamenepo, asilikali amene anabisala aja anavumbuluka pamalo pamene anali. Pa nthawi imene iye anatambasula dzanja lake, iwo anathamanga n’kukalowa mumzindawo n’kuulanda.+ Atatero, anauyatsa moto mzindawo mofulumira.+
28 Chotero Yoswa anatentha mzinda wa Ai+ n’kuusiya uli bwinja lokhalapo mpaka kalekale, ndipo lilipobe mpaka lero.