Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 32:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ifeyo tinyamula zida zathu n’kufola mwa dongosolo lomenyera nkhondo+ ndipo titsogolera ana a Isiraeli kunkhondo mpaka tikawafikitse kumalo awo. Koma ana athu aang’ono tiwasiye m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri kuti tiwateteze kwa anthu a dziko lino.

  • Numeri 32:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 mpaka dzikolo litagonjetsedwa pamaso pa Yehova.+ Pambuyo pake mudzabwerere.+ Ngati muchitadi zimenezi, mudzakhala opanda mlandu kwa Yehova ndi kwa Isiraeli. Ndipo dzikoli lidzakhaladi lanu, monga cholowa chanu pamaso pa Yehova.+

  • Deuteronomo 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 kufikira Yehova atapatsa abale anu ndi inu nomwe mpumulo, ndiponso kufikira iwo atatenga dziko limene Yehova Mulungu wanu akulipereka kwa iwo tsidya linalo la Yorodano. Mukatero mudzabwerera, aliyense kumalo ake amene ndakupatsani.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena