-
Yoswa 1:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndipo Yehova akadzapereka mpumulo kwa abale anu, monga waperekera kwa inu, nawonso abale anu akakalanda dziko limene Yehova Mulungu akuwapatsa,+ m’pamene inuyo mudzabwerere. Mudzabwerera kudziko la cholowa chanu limene Mose mtumiki wa Yehova wakugawirani,+ tsidya lino la Yorodano, kum’mawa kuno.’”+
-