Yoswa 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Malire a gawolo anatsetserekera kuchigwa cha Kana. Kenaka analowera kum’mwera kwa chigwachi kumene kuli mizinda ya Efuraimu,+ yomwe ili pakati pa mizinda ya Manase. Malire a fuko la Manasewo anali kumpoto kwa chigwachi, ndipo anakathera kunyanja.+
9 Malire a gawolo anatsetserekera kuchigwa cha Kana. Kenaka analowera kum’mwera kwa chigwachi kumene kuli mizinda ya Efuraimu,+ yomwe ili pakati pa mizinda ya Manase. Malire a fuko la Manasewo anali kumpoto kwa chigwachi, ndipo anakathera kunyanja.+