Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 27:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ngati bambo ake analibe azichimwene awo, muzipereka cholowa chake kwa wachibale wake wapafupi wa ku banja lawo,+ ndipo azitenga cholowacho kukhala chake. Ili likhale lamulo kwa ana a Isiraeli mwa chigamulo changa, monga Yehova walamulira Mose.’”

  • Numeri 36:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iwo anati: “Paja Yehova anakulamulani inu mbuyathu, kuti mugawire dzikoli ana a Isiraeli monga cholowa chawo, mwa kuchita maere.+ Yehova anakulamulaninso kuti cholowa cha m’bale wathu Tselofekadi muchipereke kwa ana ake aakazi.+

  • Numeri 36:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zimene Yehova walamula zokhudza ana aakazi a Tselofekadi+ n’zakuti, ‘Iwo angakwatiwe ndi aliyense amene wawakomera m’maso. Koma akwatiwe ndi amuna a fuko la makolo awo okha.+

  • Numeri 36:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anakwatiwa ku mabanja a ana a Manase mwana wa Yosefe, kuti cholowa chawo chisachoke ku fuko la banja la bambo awo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena