Genesis 24:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Munthuyo atamva zimenezo, anapita n’kukalowa m’nyumbamo. Pamenepo Labani anamasula ngamila ndi kuzipatsa chakudya. Anatenganso madzi n’kusambitsa mapazi a mlendoyo ndi mapazi a anyamata omwe iye anali nawo.+ Genesis 43:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano munthuyo analowetsa amunawo m’nyumba ya Yosefe. Anawapatsa madzi kuti asambe mapazi awo,+ n’kuwapatsanso chakudya choti adyetse abulu awo.+
32 Munthuyo atamva zimenezo, anapita n’kukalowa m’nyumbamo. Pamenepo Labani anamasula ngamila ndi kuzipatsa chakudya. Anatenganso madzi n’kusambitsa mapazi a mlendoyo ndi mapazi a anyamata omwe iye anali nawo.+
24 Tsopano munthuyo analowetsa amunawo m’nyumba ya Yosefe. Anawapatsa madzi kuti asambe mapazi awo,+ n’kuwapatsanso chakudya choti adyetse abulu awo.+