Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 19:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Atatero anatengera Mlevi uja kunyumba kwake+ ndipo anapatsa abulu ake aja chakudya.+ Ndiyeno anasamba mapazi awo+ n’kuyamba kudya ndi kumwa.

  • Luka 7:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Atatero anacheukira mayi uja ndi kuuza Simoni kuti: “Ukumuona kodi mayi uyu? Ngakhale kuti ndalowa m’nyumba yako, sunandipatse madzi+ otsukira mapazi anga. Koma mayi uyu wanyowetsa mapazi anga ndi misozi yake ndi kuipukuta ndi tsitsi lake.

  • 1 Timoteyo 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 wodziwika kuti anachita ntchito zabwino,+ analera bwino ana,+ anali kuchereza alendo,+ anasambitsa mapazi a oyera,+ anathandiza ena m’masautso,+ ndiponso anali kugwira mwakhama ntchito iliyonse yabwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena