Oweruza 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atafika kumzinda wa Gibeya, anapatuka kuti akalowe ndi kugona mmenemo. Ndiyeno analowa ndi kukhala pabwalo la mzindawo. Koma panalibe wowatenga kuti akagone m’nyumba yake.+ Aroma 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gawanani ndi oyera malinga ndi zosowa zawo.+ Khalani ochereza.+ Aheberi 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musaiwale kuchereza alendo,+ pakuti potero, ena anachereza angelo mosadziwa.+ 1 Petulo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muzicherezana popanda kudandaula.+
15 Atafika kumzinda wa Gibeya, anapatuka kuti akalowe ndi kugona mmenemo. Ndiyeno analowa ndi kukhala pabwalo la mzindawo. Koma panalibe wowatenga kuti akagone m’nyumba yake.+