Genesis 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Loti anawaumiriza kwambiri+ moti mpaka iwo anapita naye kunyumba kwake. Kumeneko anawakonzera phwando,+ n’kuwaphikira mikate yopanda chofufumitsa,+ ndipo anadya. Machitidwe 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano iye ndi a m’banja lake atabatizidwa,+ anachonderera kuti: “Abale ngati inu mwaona kuti ndine wokhulupirika kwa Yehova, tiyeni mukalowe m’nyumba yanga ndi kukhala mmenemo.”+ Moti anatiumiriza ndithu kupita kwawo.+
3 Koma Loti anawaumiriza kwambiri+ moti mpaka iwo anapita naye kunyumba kwake. Kumeneko anawakonzera phwando,+ n’kuwaphikira mikate yopanda chofufumitsa,+ ndipo anadya.
15 Tsopano iye ndi a m’banja lake atabatizidwa,+ anachonderera kuti: “Abale ngati inu mwaona kuti ndine wokhulupirika kwa Yehova, tiyeni mukalowe m’nyumba yanga ndi kukhala mmenemo.”+ Moti anatiumiriza ndithu kupita kwawo.+