Oweruza 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzu ndi chakudya+ china cha abulu athu tili nazo, ndipo tilinso ndi mkate+ ndi vinyo wa ine ndi kapolo wanu wamkazi+ komanso wa mtumiki+ wa kapolo wanu. Sitikusowa kanthu.”
19 Udzu ndi chakudya+ china cha abulu athu tili nazo, ndipo tilinso ndi mkate+ ndi vinyo wa ine ndi kapolo wanu wamkazi+ komanso wa mtumiki+ wa kapolo wanu. Sitikusowa kanthu.”