Genesis 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma iwo asanagone, amuna a mumzindamo, amuna a mu Sodomu, anafika n’kuzungulira nyumbayo.+ Anafika ali chigulu, kuyambira tianyamata mpaka nkhalamba.+ Oweruza 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anthu a m’Gibeya anayamba kundiukira, ndipo usiku anazungulira nyumba imene ndinalimo. Iwo anali kufuna kupha ineyo, koma anagwirira mdzakazi wanga+ mpaka anafa.+
4 Koma iwo asanagone, amuna a mumzindamo, amuna a mu Sodomu, anafika n’kuzungulira nyumbayo.+ Anafika ali chigulu, kuyambira tianyamata mpaka nkhalamba.+
5 Ndiyeno anthu a m’Gibeya anayamba kundiukira, ndipo usiku anazungulira nyumba imene ndinalimo. Iwo anali kufuna kupha ineyo, koma anagwirira mdzakazi wanga+ mpaka anafa.+