18 Poyankha anamuuza kuti: “Tikudutsa kuchokera ku Betelehemu wa ku Yuda kupita kudera lamapiri lakutali kwambiri la Efuraimu.+ Kumeneko ndiye kwathu, koma ndinapita ku Betelehemu wa ku Yuda.+ Panopa ndikupita kunyumba kwanga, koma palibe amene akunditenga kuti ndikagone m’nyumba yake.+