Oweruza 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zitatero, ana a Benjamini anatuluka m’Gibeya+ ndi kupha amuna a Isiraeli 22,000 tsiku limenelo, n’kusiya mitembo yawo itagonagona pansi.+
21 Zitatero, ana a Benjamini anatuluka m’Gibeya+ ndi kupha amuna a Isiraeli 22,000 tsiku limenelo, n’kusiya mitembo yawo itagonagona pansi.+