Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 26:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Amenewa ndiwo anali ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 45,600.+

  • Oweruza 20:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiyeno ana a Benjamini anasonkhana pamodzi ku Gibeya, kuchokera m’mizinda, kuti akamenyane ndi ana a Isiraeli.

  • Oweruza 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Masiku amenewo Pinihasi,+ mwana wa Eleazara, mwana wa Aroni, ndiye anali kuimirira pafupi ndi likasalo.+ Chotero iye anafunsa kuti: “Kodi ndipitenso kukamenyana ndi ana a m’bale wanga Benjamini kapena ndisapite?”+ Poyankha, Yehova anati: “Pita, chifukwa mawa ndim’pereka m’dzanja lako.”+

  • Oweruza 20:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Amuna a Isiraeli anabwerera kukaukira ana a Benjamini ndipo anakantha ndi lupanga zonse za m’mizinda, kuyambira anthu mpaka ziweto, ndi chilichonse chimene anapeza.+ Kuwonjezera apo, mizinda yonse imene anaipeza anaiyatsa moto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena