Ekisodo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Aamaleki+ anabwera kudzamenyana ndi Isiraeli ku Refidimu.+ Oweruza 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Aisiraeli akalima minda yawo,+ Amidiyani, Aamaleki+ ndi anthu a Kum’mawa+ anali kubwera kudzawaukira. Salimo 83:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Agebala, Aamoni,+ Aamaleki,Afilisiti+ pamodzi ndi anthu a ku Turo.+
3 Ndiyeno Aisiraeli akalima minda yawo,+ Amidiyani, Aamaleki+ ndi anthu a Kum’mawa+ anali kubwera kudzawaukira.