1 Mbiri 2:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 M’kupita kwa nthawi anabereka Safa bambo wa Madimana.+ Anaberekanso Seva bambo wa Makibena ndi Gibeya.+ Mwana wamkazi wa Kalebe+ anali Akisa.+
49 M’kupita kwa nthawi anabereka Safa bambo wa Madimana.+ Anaberekanso Seva bambo wa Makibena ndi Gibeya.+ Mwana wamkazi wa Kalebe+ anali Akisa.+