Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 22:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Kodi Yehova Mulungu wanu sali nanu?+ Kodi sanakupatseni mpumulo m’dziko lonseli?+ Pakuti iye wapereka m’manja mwanga anthu a m’dzikoli, ndipo dzikoli lagonjetsedwa pamaso pa Yehova+ ndi pa anthu ake.

  • Nehemiya 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Choncho ana awo+ analowa ndi kutenga dzikolo,+ ndipo munagonjetsa+ anthu okhala m’dzikolo, Akanani,+ ndi kuwapereka m’manja mwawo. Munaperekanso ngakhale mafumu a Akananiwo+ ndi mitundu ya anthu ya m’dzikolo+ kwa ana a Isiraeliwo kuti awachite zimene akufuna.+

  • Salimo 18:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Mulungu woona ndiye Wobwezera adani anga.+

      Iye amagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuiika kunsi kwa mapazi anga.+

  • Salimo 47:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye adzagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuiika pansi pathu.+

      Adzagonjetsa anthu a mitundu ina ndi kuwaika pansi pa mapazi athu.+

  • Salimo 81:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndikanagonjetsa adani awo mosavuta,+

      Ndipo ndikanalanga adani awo ndi dzanja langa.+

  • Aheberi 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Mwa chikhulupiriro, anthu amenewa anagonjetsa maufumu pa nkhondo,+ anachita chilungamo,+ analandira malonjezo+ ndiponso anatseka mikango pakamwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena