Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Koma khalani tcheru ndipo musamale moyo wanu,+ kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona,+ ndi kuti mitima yanu isaiwale zinthu zimenezo masiku onse a moyo wanu.+ Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauza za zinthu zimenezo,+

  • Deuteronomo 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 ndi kuwakhomereza mwa ana ako.+ Uzilankhula nawo za mawuwo ukakhala pansi m’nyumba mwako, poyenda pamsewu, pogona+ ndi podzuka.

  • Salimo 44:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,

      Makolo athu anatifotokozera+

      Ntchito zimene inu munachita m’masiku awo,+

      M’masiku akale.+

  • Salimo 78:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Amene tinamva ndipo tikuwadziwa,+

      Komanso amene makolo athu anatifotokozera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena