Oweruza 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma poyankha, akalonga a ku Sukoti anati: “Tipatsirenji asilikali ako mkate ngati kuti wagwira kale Zeba ndi Zalimuna?”+ Miyambo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+
6 Koma poyankha, akalonga a ku Sukoti anati: “Tipatsirenji asilikali ako mkate ngati kuti wagwira kale Zeba ndi Zalimuna?”+
27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+