Genesis 31:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Labani anapitiriza kulankhula kuti: “Mulu wa miyalawu ndi mboni yathu lero pakati pa ine ndi iwe.” N’chifukwa chake unatchedwa Galeeda,+ Numeri 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye anawauza kuti: “Ana a Gadi ndi ana a Rubeni akawoloka nanu Yorodano, aliyense wokonzekera kukamenya nkhondo+ pamaso pa Yehova, ndipo ngati dzikolo lidzagonjetsedwa pamaso panu, pamenepo mudzawapatse dziko la Giliyadi monga cholowa chawo.+
48 Labani anapitiriza kulankhula kuti: “Mulu wa miyalawu ndi mboni yathu lero pakati pa ine ndi iwe.” N’chifukwa chake unatchedwa Galeeda,+
29 Iye anawauza kuti: “Ana a Gadi ndi ana a Rubeni akawoloka nanu Yorodano, aliyense wokonzekera kukamenya nkhondo+ pamaso pa Yehova, ndipo ngati dzikolo lidzagonjetsedwa pamaso panu, pamenepo mudzawapatse dziko la Giliyadi monga cholowa chawo.+