Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndipo Yehova akadzapereka mpumulo kwa abale anu, monga waperekera kwa inu, nawonso abale anu akakalanda dziko limene Yehova Mulungu akuwapatsa,+ m’pamene inuyo mudzabwerere. Mudzabwerera kudziko la cholowa chanu limene Mose mtumiki wa Yehova wakugawirani,+ tsidya lino la Yorodano, kum’mawa kuno.’”+

  • Yoswa 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano Mose anagawira dziko ana a Rubeni potsata mabanja awo.

  • Yoswa 13:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kenako Mose anagawira dziko fuko la ana a Gadi potsata mabanja awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena