Genesis 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yakobo anathawa n’kuwoloka Mtsinje*+ limodzi ndi zonse zimene anali nazo. Atatero, anayenda molunjika dera la kumapiri la Giliyadi.+ Numeri 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye anawauza kuti: “Ana a Gadi ndi ana a Rubeni akawoloka nanu Yorodano, aliyense wokonzekera kukamenya nkhondo+ pamaso pa Yehova, ndipo ngati dzikolo lidzagonjetsedwa pamaso panu, pamenepo mudzawapatse dziko la Giliyadi monga cholowa chawo.+
21 Yakobo anathawa n’kuwoloka Mtsinje*+ limodzi ndi zonse zimene anali nazo. Atatero, anayenda molunjika dera la kumapiri la Giliyadi.+
29 Iye anawauza kuti: “Ana a Gadi ndi ana a Rubeni akawoloka nanu Yorodano, aliyense wokonzekera kukamenya nkhondo+ pamaso pa Yehova, ndipo ngati dzikolo lidzagonjetsedwa pamaso panu, pamenepo mudzawapatse dziko la Giliyadi monga cholowa chawo.+