Oweruza 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo akulu a ku Giliyadi anayankha Yefita kuti: “Eya, n’chifukwa chake tsopano tabwerera+ kwa iwe. Choncho upite nafe kukamenyana ndi ana a Amoni, ndipo ukhale mtsogoleri wa anthu onse okhala ku Giliyadi.”+
8 Pamenepo akulu a ku Giliyadi anayankha Yefita kuti: “Eya, n’chifukwa chake tsopano tabwerera+ kwa iwe. Choncho upite nafe kukamenyana ndi ana a Amoni, ndipo ukhale mtsogoleri wa anthu onse okhala ku Giliyadi.”+