Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 24:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mwana wa mkaziyo anali wokongola mochititsa kaso,+ ndipo anali namwali amene anali asanagonepo ndi mwamuna.+ Iye analowa m’chitsimemo n’kutunga madzi mumtsuko wake, kenako anatulukamo.

  • Genesis 30:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Rakele anakhala ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna. Ndiyeno iye anati: “Mulungu wandichotsera chitonzo.”+

  • Rute 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Zitatero akazi anayamba kuuza+ Naomi kuti: “Adalitsike Yehova,+ amene wachititsa kuti usasowe wokuwombola lero, kuti dzina lake lifalitsidwe mu Isiraeli.

  • 1 Samueli 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mkazi mnzake wa Hana anali kum’sautsa+ kwambiri n’cholinga choti amukhumudwitse, chifukwa chakuti Yehova anali atatseka mimba yake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena