Oweruza 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Atamaliza kulankhula zimenezi, nthawi yomweyo anataya fupa lija ndi kutcha malowo kuti Ramati-lehi.*+ Oweruza 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero Mulungu anang’amba nthaka ku Lehi ndipo madzi+ anayamba kutuluka panthakapo. Pamenepo Samisoni anamwa madziwo, moti anapezanso mphamvu+ ndi kutsitsimulidwa.+ N’chifukwa chake anatcha malowo kuti Eni-hakore.* Malo amenewa ali ku Lehi kufikira lero. 2 Samueli 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Womutsatira anali Shama, mwana wamwamuna wa Age Mharari.+ Tsopano Afilisiti anasonkhana pamodzi ku Lehi, kumene kunali munda wodzaza ndi mphodza.+ Kumeneko anthu anali atathawa chifukwa choopa Afilisitiwo.
17 Atamaliza kulankhula zimenezi, nthawi yomweyo anataya fupa lija ndi kutcha malowo kuti Ramati-lehi.*+
19 Chotero Mulungu anang’amba nthaka ku Lehi ndipo madzi+ anayamba kutuluka panthakapo. Pamenepo Samisoni anamwa madziwo, moti anapezanso mphamvu+ ndi kutsitsimulidwa.+ N’chifukwa chake anatcha malowo kuti Eni-hakore.* Malo amenewa ali ku Lehi kufikira lero.
11 Womutsatira anali Shama, mwana wamwamuna wa Age Mharari.+ Tsopano Afilisiti anasonkhana pamodzi ku Lehi, kumene kunali munda wodzaza ndi mphodza.+ Kumeneko anthu anali atathawa chifukwa choopa Afilisitiwo.