Numeri 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anauza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti: “Dziko limene tinakalowamo n’kulizonda, n’labwino kwambiri.+ Deuteronomo 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Yehova Mulungu wanu akukulowetsani m’dziko labwino,+ dziko la zigwa* za madzi,+ akasupe ndi madzi ochuluka otuluka m’zigwa ndi m’madera a mapiri,
7 Iwo anauza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti: “Dziko limene tinakalowamo n’kulizonda, n’labwino kwambiri.+
7 Pakuti Yehova Mulungu wanu akukulowetsani m’dziko labwino,+ dziko la zigwa* za madzi,+ akasupe ndi madzi ochuluka otuluka m’zigwa ndi m’madera a mapiri,